-
Yeremiya 34:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Inu simunamvere mawu anga oti mulengeze ufulu, aliyense kwa mʼbale wake ndi kwa mnzake.+ Tsopano ine ndikulengeza ufulu kwa inu,’ akutero Yehova. ‘Inu mudzafa ndi lupanga, mliri* ndi njala.+ Ndidzakusandutsani chinthu chimene maufumu onse apadziko lapansi adzachita nacho mantha.+
-