Ekisodo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+ Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+ Deuteronomo 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ngati anakugulitsa m’bale wako, Mheberi wamwamuna kapena wamkazi,+ ndipo wakutumikira zaka 6, m’chaka cha 7 uzim’masula ndi kumulola kuchoka.+
2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
12 “Ngati anakugulitsa m’bale wako, Mheberi wamwamuna kapena wamkazi,+ ndipo wakutumikira zaka 6, m’chaka cha 7 uzim’masula ndi kumulola kuchoka.+