14 “Kumapeto kwa zaka 7, aliyense wa inu, azimasula m’bale wake,+ Mheberi+ amene anagulitsidwa kwa inu+ ndiponso amene wakutumikirani kwa zaka 6. Muzimulola kuchoka mwaufulu kuti apite kwawo.” Koma makolo anu sanandimvere ndipo sanatchere khutu lawo.+