Yeremiya 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kumapeto kwa zaka 7, aliyense wa inu azimasula mʼbale wake yemwe ndi Mheberi amene anagulitsidwa kwa inu ndipo wakutumikirani kwa zaka 6. Muzimulola kuti achoke.”+ Koma makolo anu sanandimvere ndipo sanatchere khutu lawo.
14 “Kumapeto kwa zaka 7, aliyense wa inu azimasula mʼbale wake yemwe ndi Mheberi amene anagulitsidwa kwa inu ndipo wakutumikirani kwa zaka 6. Muzimulola kuti achoke.”+ Koma makolo anu sanandimvere ndipo sanatchere khutu lawo.