Ekisodo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+ Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu n’kudzigulitsa kwa inu,+ musam’gwiritse ntchito ngati kapolo.+
2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+