-
2 Mafumu 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mayi wina yemwe anali mmodzi wa akazi a ana+ a aneneri, anafika kwa Elisa n’kulankhula mokweza kuti: “Mtumiki wanu yemwe anali mwamuna wanga anamwalira. Inu mukudziwa bwino kuti mtumiki wanuyo anali woopa+ Yehova. Tsopano kwabwera wangongole+ kudzatenga ana anga onse awiri kuti akakhale akapolo ake.”
-
-
Nehemiya 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Komatu ife ndi anzathuwo ndife pachibale.+ Ana athu aamuna n’chimodzimodzi ndi ana awo aamuna, koma ife tikusandutsa ana athu aamuna ndi ana athu aakazi kukhala akapolo.+ Ndipotu ena mwa ana athu aakazi tawasandutsa kale akapolo. Ife tilibenso mphamvu, chifukwa minda yathu ya tirigu ndi minda yathu ya mpesa ili m’manja mwa anthu ena.”
-