Ekisodo 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+ Levitiko 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 M’chaka chimenecho iye ndi ana ake amasuke ndi kubwerera kwa achibale ake. Abwerere kumalo a makolo ake.+
2 “Ukagula kapolo wachiheberi,+ adzakhala kapolo wako kwa zaka 6, koma m’chaka cha 7 azimasuka ndipo azichoka osam’lipiritsa.+
41 M’chaka chimenecho iye ndi ana ake amasuke ndi kubwerera kwa achibale ake. Abwerere kumalo a makolo ake.+