Levitiko 25:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu n’kudzigulitsa kwa inu,+ musam’gwiritse ntchito ngati kapolo.+