Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 146:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+

      Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+

      Yehova amamasula anthu omangidwa.+

  • Yesaya 61:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Mzimu wa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, uli pa ine,+ pakuti Yehova wandidzoza+ kuti ndikanene uthenga wabwino kwa anthu ofatsa.+ Wandituma kuti ndikamange zilonda za anthu osweka mtima,+ ndikalengeze za ufulu kwa anthu ogwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,+ ndiponso ndikatsegule maso a akaidi.+

  • Yesaya 63:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti tsiku lobwezera lili mumtima mwanga,+ ndipo chaka choti anthu anga awomboledwe chafika.

  • Yeremiya 34:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehova anauza Yeremiya mawu pamene Mfumu Zedekiya inachita pangano ndi anthu onse a mu Yerusalemu kuti alengeze ufulu,+

  • Luka 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Mzimu wa Yehova+ uli pa ine, chifukwa iye anandidzoza kuti ndilengeze uthenga wabwino kwa osauka. Anandituma kudzalalikira za kumasulidwa kwa ogwidwa ukapolo, ndi zoti akhungu ayambe kuona. Anandituma kudzamasula oponderezedwa kuti akhale mfulu,+

  • Aroma 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 chakuti chilengedwecho+ chidzamasulidwa+ ku ukapolo wa kuvunda n’kukhala ndi ufulu waulemerero wa ana a Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena