Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Machitidwe 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+ Machitidwe 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+
38 Nkhani yake inali yonena za Yesu wa ku Nazareti, kuti Mulungu anamudzoza ndi mzimu woyera+ ndi mphamvu. Ndiponso kuti popeza Mulungu anali naye,+ anayendayenda m’dziko, n’kumachita zabwino ndi kuchiritsa onse osautsidwa ndi Mdyerekezi.+