Salimo 48:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Taonani! Mafumu anakumana atapangana,+Koma anangodutsa.+ Luka 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mu ola lomwelo kunafika Afarisi ena ndi kumuuza kuti: “Nyamukani muchoke kuno, chifukwa Herode* akufuna kukuphani.” Luka 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Herode pamodzi ndi asilikali ake omulondera anamupeputsa.+ Anamuchitira zachipongwe+ mwa kumuveka chovala chonyezimira ndipo anamutumizanso kwa Pilato. Chivumbulutso 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ndinaona chilombo,+ mafumu+ a dziko lapansi, ndi magulu awo ankhondo atasonkhana pamodzi kuti amenyane+ ndi wokwera pahatchi+ uja ndi gulu lake lankhondo.
31 Mu ola lomwelo kunafika Afarisi ena ndi kumuuza kuti: “Nyamukani muchoke kuno, chifukwa Herode* akufuna kukuphani.”
11 Pamenepo Herode pamodzi ndi asilikali ake omulondera anamupeputsa.+ Anamuchitira zachipongwe+ mwa kumuveka chovala chonyezimira ndipo anamutumizanso kwa Pilato.
19 Ndipo ndinaona chilombo,+ mafumu+ a dziko lapansi, ndi magulu awo ankhondo atasonkhana pamodzi kuti amenyane+ ndi wokwera pahatchi+ uja ndi gulu lake lankhondo.