Mateyu 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+ Maliko 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi a chipani cha Herode+ kuti amuphe.+
27 M’mawa kutacha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu onse anakambirana ndi kugwirizana kuti aphe Yesu.+
6 Ataona zimenezi Afarisiwo anatuluka ndipo nthawi yomweyo anapita kukakonza chiwembu limodzi ndi a chipani cha Herode+ kuti amuphe.+