Salimo 103:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova akuchitira chilungamo+Ndi kuperekera zigamulo anthu amene akuchitiridwa zachinyengo.+