Salimo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+ Salimo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+ Salimo 71:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+ Salimo 146:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+
8 Inu Yehova, nditsogolereni m’chilungamo chanu+ chifukwa adani anga andizungulira.+Salazani njira yanu kuti ndiyendemo popanda chopunthwitsa.+
2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+
7 Iye ndi Woperekera chiweruzo anthu ochitiridwa chinyengo,+Wopereka chakudya kwa anthu anjala.+Yehova amamasula anthu omangidwa.+