Salimo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+ Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+
6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+