Salimo 55:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine ndidzafuulira Mulungu.+Ndipo Yehova adzandipulumutsa.+ Salimo 66:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndithudi, Mulungu wamva,+Wamvetsera mwatcheru mawu a pemphero langa.+