Salimo 107:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anawatulutsa mu mdima, mu mdima wandiweyani,+Ndi kudula zingwe zimene anamangidwa nazo.+ Salimo 142:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+
7 Nditulutseni mundende ya mdima+Kuti nditamande dzina lanu.+Chititsani kuti anthu olungama asonkhane ndi kundizungulira,+Chifukwa mumandichitira zabwino.+