Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 68:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mulungu akuchititsa osungulumwa kukhala m’nyumba.+

      Akumasula akaidi ndi kuwathandiza kuti zinthu ziwayendere bwino.+

      Koma anthu osamvera adzakhala m’dziko lowonongeka ndi kutentha kwa dzuwa.+

  • Yesaya 49:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 kuti ndiuze akaidi+ kuti, ‘Tulukani!’+ ndi amene ali mu mdima+ kuti, ‘Dziululeni!’+ Iwo adzadya msipu m’mphepete mwa msewu, ndipo m’mphepete mwa njira zonse zodutsidwadutsidwa mudzakhala malo awo odyeramo msipu.+

  • Aefeso 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pakuti poyamba munali mdima,+ koma tsopano ndinu kuwala+ mogwirizana ndi Ambuye. Yendanibe ngati ana a kuwala.

  • 1 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena