Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba. Yohane 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani chikhulupiriro mwa kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka ndi kuwabisalira. 1 Yohane 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene amanena kuti ali m’kuunika koma amadana+ ndi m’bale wake, ndiye kuti ali mu mdima mpaka pano.+
16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba.
36 Pamene kuwala mudakali nako, sonyezani chikhulupiriro mwa kuwalako, kuti mukhale ana ake a kuwala.”+ Yesu atanena zimenezi, anachoka ndi kuwabisalira.
9 Amene amanena kuti ali m’kuunika koma amadana+ ndi m’bale wake, ndiye kuti ali mu mdima mpaka pano.+