Salimo 68:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu amene alibe wowathandiza, Mulungu amawapatsa nyumba kuti azikhalamo.+Amamasula akaidi nʼkuwathandiza kuti zinthu ziwayendere bwino.+ Koma anthu osamvera* adzakhala mʼdziko louma.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 68:6 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 1 2018, tsa. 11
6 Anthu amene alibe wowathandiza, Mulungu amawapatsa nyumba kuti azikhalamo.+Amamasula akaidi nʼkuwathandiza kuti zinthu ziwayendere bwino.+ Koma anthu osamvera* adzakhala mʼdziko louma.+