Deuteronomo 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+ Deuteronomo 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wanu lidzakhala ngati kopa,* ndipo nthaka yanu idzakhala ngati chitsulo.+ Salimo 107:33, 34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lopanda chonde,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo.
15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+
23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wanu lidzakhala ngati kopa,* ndipo nthaka yanu idzakhala ngati chitsulo.+
33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo ouma.+34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lopanda chonde,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo.