Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+ Yesaya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+ Luka 1:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”
4 Waunika mu mdima kuti anthu owongoka mtima aone kuwala.+ ח [Chehth]Iye ndi wachisomo, wachifundo ndi wolungama.+
2 Anthu amene anali kuyenda mu mdima, aona kuwala kwakukulu.+ Anthu amene anali kukhala m’dziko la mdima wandiweyani,+ kuwala kwawawalira.+
79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”