Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wapereka madzi kwa anthu aludzu.+Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+ Salimo 145:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumatambasula dzanja lanu+Ndi kukhutiritsa zokhumba za chamoyo chilichonse.+