Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti iye wapereka madzi kwa anthu aludzu.+Ndipo anthu anjala wawadyetsa zinthu zabwino.+ Salimo 132:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndithu ndidzadalitsa chakudya chake.+Anthu ake osauka ndidzawapatsa chakudya chokwanira.+