Salimo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ofatsa adzadya ndi kukhuta.+Ofunafuna Yehova adzamutamanda.+Mitima yanu ikhale ndi moyo kosatha.+ Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+