Levitiko 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati wapereka mundawo kuyambira m’Chaka cha Ufulu+ kupita m’tsogolo, mtengo wake woikidwiratu uzikhala womwewo, wogwirizana ndi mbewu. Levitiko 27:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 M’Chaka cha Ufulu mundawo udzabwezedwa kwa mwiniwake weniweni amene anaugulitsa.+
17 Ngati wapereka mundawo kuyambira m’Chaka cha Ufulu+ kupita m’tsogolo, mtengo wake woikidwiratu uzikhala womwewo, wogwirizana ndi mbewu.