Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+ Levitiko 25:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye aziwerengera wom’gulayo zaka zotsala kuchokera pamene anadzigulitsa kukafika Chaka cha Ufulu,+ ndipo ndalama zimene anam’gulira zizigwirizana ndi kuchuluka kwa zaka.+ Azim’gwirira ntchito mofanana ndi waganyu.+
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
50 Iye aziwerengera wom’gulayo zaka zotsala kuchokera pamene anadzigulitsa kukafika Chaka cha Ufulu,+ ndipo ndalama zimene anam’gulira zizigwirizana ndi kuchuluka kwa zaka.+ Azim’gwirira ntchito mofanana ndi waganyu.+