Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+ Levitiko 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.
10 Chaka cha 50 chizikhala chopatulika, ndipo muzilengeza ufulu* kwa anthu onse okhala m’dzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu+ kwa inu, ndipo aliyense wa inu azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+
16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.