-
Levitiko 25:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ngati patsala zaka zambiri, angathe kukweza mtengo wogulitsira malowo, koma ngati patsala zaka zochepa, azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa kuchuluka kwa mbewu zimene udzakolole.
-