Levitiko 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.
16 Ngati zaka zimene udzakhala ukukololapo n’zambiri, azikugulitsa pa mtengo wokwera,+ koma ngati zakazo zili zochepa azitsitsa mtengo wa malowo, chifukwa akukugulitsa mbewu zimene udzakhala ukukololapo.