Deuteronomo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zisakhale zovuta kwa iwe kum’masula kuti achoke,+ chifukwa wakutumikira zaka 6, moti malipiro ake akanafanana ndi malipiro a anthu awiri aganyu,+ ndipo Yehova Mulungu wako wakudalitsa pa chilichonse chimene wachita.+ Yesaya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+ Yesaya 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.
18 Zisakhale zovuta kwa iwe kum’masula kuti achoke,+ chifukwa wakutumikira zaka 6, moti malipiro ake akanafanana ndi malipiro a anthu awiri aganyu,+ ndipo Yehova Mulungu wako wakudalitsa pa chilichonse chimene wachita.+
14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+
16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.