Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+

  • Salimo 120:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+

      Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+

  • Nyimbo ya Solomo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Inu ana aakazi a ku Yerusalemu,+ ine ndine mtsikana wakuda ngati mahema a ku Kedara,+ koma wokongola ngati nsalu za mahema+ a Solomo.

  • Yesaya 42:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chipululu+ ndi mizinda ya kumeneko, ndiponso midzi ya ku Kedara zikweze mawu awo.+ Anthu okhala m’dera lamatanthwe+ afuule mokondwera. Anthu afuule kuchokera pamwamba pa mapiri.

  • Ezekieli 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena