Salimo 45:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+
9 Ana aakazi+ a mafumu ali m’gulu la akazi ako okondedwa.Mkazi wamkulu wa mfumu+ waima kudzanja lako lamanja atavala zovala zagolide wa ku Ofiri.+