Genesis 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+ Salimo 120:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+ Yesaya 60:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira.+ Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+ ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yokongola.+
13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+
5 Tsoka kwa ine! Chifukwa ndakhala mlendo m’dziko la Meseke.+Ndakhala muhema pakati pa mahema a Kedara.+
7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe. Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira.+ Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+ ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yokongola.+