Genesis 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mukudziwa kuti ine ndisanabwere munali ndi zochepa. Tsopano onani mmene Yehova wakudalitsirani ndi mmene zachulukira kuchokera pamene ndinabwera.+ Ndiye kodi ineyo ndidzayamba liti kugwirira ntchito banja langa?”+
30 Mukudziwa kuti ine ndisanabwere munali ndi zochepa. Tsopano onani mmene Yehova wakudalitsirani ndi mmene zachulukira kuchokera pamene ndinabwera.+ Ndiye kodi ineyo ndidzayamba liti kugwirira ntchito banja langa?”+