Genesis 32:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+ 1 Timoteyo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.
10 Ine ndine wosayenerera kukoma mtima kosatha ndi kukhulupirika konseku, kumene mwandionetsa ine mtumiki wanu.+ Ndinawoloka Yorodano ndilibe kanthu, koma ndodo yokha, ndipo tsopano ndili ndi magulu awiriwa.+
8 Ndithudi, ngati munthu sasamalira anthu amene ndi udindo wake kuwasamalira,+ makamaka a m’banja lake,+ wakana+ chikhulupiriro+ ndipo ndi woipa kuposa munthu wosakhulupirira.