Genesis 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndili nawe ndipo ndikuyang’anira pa ulendo wako wonse, kufikira ndidzakubwezera kumalo ano.+ Sindidzakusiya kufikira nditachitadi zimene ndanena kwa iwe.”+ Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Mika 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+
15 Ine ndili nawe ndipo ndikuyang’anira pa ulendo wako wonse, kufikira ndidzakubwezera kumalo ano.+ Sindidzakusiya kufikira nditachitadi zimene ndanena kwa iwe.”+
5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
20 Zonse zimene munanena kwa Yakobo zinali zoona ndipo Abulahamu munamusonyeza kukoma mtima kosatha. Ifenso mudzatichitira zomwezo chifukwa n’zimene munalonjeza makolo athu kalekale.+