Genesis 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye. Genesis 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+
6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye.
4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+