Genesis 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Yakobo anafika ku Luzi,+ komwe ndi ku Beteli, mʼdziko la Kanani. Iye anafika kumeneko limodzi ndi anthu onse amene anali naye.
6 Kenako Yakobo anafika ku Luzi,+ komwe ndi ku Beteli, mʼdziko la Kanani. Iye anafika kumeneko limodzi ndi anthu onse amene anali naye.