Genesis 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye.
6 Potsirizira pake Yakobo anafika ku Luzi+ komwe ndi ku Beteli, m’dziko la Kanani. Iye anafika kumeneko pamodzi ndi anthu onse amene anali naye.