Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa Yehova ndi wabwino.+Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwo yonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 100:5 Nsanja ya Olonda,1/15/1995, ptsa. 19-20
5 Chifukwa Yehova ndi wabwino.+Chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwo yonse.+