Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+ 7 Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa mibadwo masauzande,+ amakhululuka zolakwa ndi machimo,+ koma sadzalekerera wolakwa osamʼpatsa chilango.+ Amalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+

  • Deuteronomo 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Inu mukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu woona, Mulungu wokhulupirika, amene amasunga pangano lake ndiponso amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amamukonda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo 1,000.+

  • Salimo 98:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Iye wakumbukira chikondi chake chokhulupirika komanso kukhulupirika kumene analonjeza nyumba ya Isiraeli.+

      Anthu onse padziko lapansi aona mmene Mulungu wathu wapulumutsira anthu ake.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena