Yeremiya 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+ Mika 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+
3 Yehova anaonekera kwa ine ali kutali ndipo anati: “Ine ndakukonda ndipo ndidzakukonda mpaka kalekale. Nʼchifukwa chake ndakukokera kwa ine ndi chikondi chokhulupirika.*+
22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+Ndipo chifundo chake sichitha.+
18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu,Amene amakhululukira zolakwa ndi machimo+ a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale,Chifukwa mumakonda chikondi chokhulupirika.+