Yesaya 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa izi ndi zimene Yehova anandiuza: “Chaka chimodzi chisanathe, mofanana ndi zaka za munthu waganyu,* ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:16 Yesaya 1, ptsa. 228-229
16 Chifukwa izi ndi zimene Yehova anandiuza: “Chaka chimodzi chisanathe, mofanana ndi zaka za munthu waganyu,* ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.