Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mayina a ana a Isimaeli, malinga ndi mabanja awo ndi awa: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+

  • Salimo 120:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Tsoka kwa ine, chifukwa ndakhala mʼdziko la Meseki+ ngati mlendo.

      Ndimakhala mutenti pakati pa matenti a ku Kedara.+

  • Nyimbo ya Solomo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Inu ana aakazi a ku Yerusalemu, ine ndine wakuda koma wokongola,

      Ngati matenti a ku Kedara+ komanso nsalu za matenti+ a Solomo.

  • Yesaya 42:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chipululu ndi mizinda yake zifuule+

      Komanso midzi imene kumakhala Akedara.+

      Anthu amene amakhala mʼdera lamatanthwe afuule mosangalala.

      Anthuwo afuule kuchokera pamwamba pa mapiri.

  • Yeremiya 49:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a ku Hazori amene Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inawagonjetsa, Yehova wanena kuti:

      “Nyamukani, pitani ku Kedara,

      Ndipo mukawononge ana a Kumʼmawa.

  • Ezekieli 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Unalemba ntchito Aluya ndi atsogoleri onse a ku Kedara,+ amene ankagulitsa ana a nkhosa, nkhosa zamphongo ndi mbuzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena