Yesaya 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:16 Yesaya 1, ptsa. 228-229
16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.