Yobu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kodi si paja munthu amagwira ntchito yokakamiza+ padziko lapansi?Ndipo kodi masiku ake sali ngati masiku a munthu waganyu?+ Yesaya 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+
7 “Kodi si paja munthu amagwira ntchito yokakamiza+ padziko lapansi?Ndipo kodi masiku ake sali ngati masiku a munthu waganyu?+
14 Koma tsopano Yehova wanena kuti: “Pomatha ndendende zaka zitatu,*+ ulemerero+ wa Mowabu udzatha. Iye adzachititsidwa manyazi ndipo adzakumana ndi chipwirikiti chamtundu uliwonse. Otsala mwa iye adzakhala ochepa kwambiri ndiponso opanda mphamvu.”+