Yesaya 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.
16 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Pakutha chaka chimodzi, osawonjezerapo ngakhale tsiku limodzi,*+ ulemerero wonse wa Kedara+ udzakhala utatha.