Levitiko 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
34 “‘Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhala bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli m’dziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzasunga sabata ndipo lidzabweza masabata ake.+
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.