Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+

      Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+

      Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+

      Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+

  • Yeremiya 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+

  • Yeremiya 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Tichoke kupita kuti?’ ukayankhe kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Woyenera kufa ndi mliri afe ndi mliri! Woyenera kufa ndi lupanga afe ndi lupanga! Woyenera kufa ndi njala yaikulu afe ndi njala yaikulu!+ Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo atengedwe kupita ku ukapolo!”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena